Esitere 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Hamani ataona kuti Moredikayi sankamuweramira ndiponso kumugwadira, anakwiya kwambiri.+