Esitere 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno mʼmwezi woyamba, umene ndi mwezi wa Nisani,* mʼchaka cha 12+ cha Mfumu Ahasiwero, anthu anachita Puri+ kapena kuti maere pamaso pa Hamani kuti adziwe tsiku ndi mwezi woyenerera. Maerewo anagwera mwezi wa 12 umene ndi mwezi wa Adara.*+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2136, 2244 Nsanja ya Olonda,3/15/1986, tsa. 24
7 Ndiyeno mʼmwezi woyamba, umene ndi mwezi wa Nisani,* mʼchaka cha 12+ cha Mfumu Ahasiwero, anthu anachita Puri+ kapena kuti maere pamaso pa Hamani kuti adziwe tsiku ndi mwezi woyenerera. Maerewo anagwera mwezi wa 12 umene ndi mwezi wa Adara.*+