Esitere 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moredikayi+ atadziwa zonse zimene zinachitika,+ anangʼamba zovala zake nʼkuvala chiguduli ndipo anadzithira phulusa. Kenako anapita pakati pa mzinda nʼkuyamba kulira mofuula ndiponso mopwetekedwa mtima. Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Tsanzirani, ptsa. 131-132 Nsanja ya Olonda,10/1/2011, tsa. 21
4 Moredikayi+ atadziwa zonse zimene zinachitika,+ anangʼamba zovala zake nʼkuvala chiguduli ndipo anadzithira phulusa. Kenako anapita pakati pa mzinda nʼkuyamba kulira mofuula ndiponso mopwetekedwa mtima.