Esitere 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo mʼzigawo zonse+ kumene kunafika mawu a mfumu ndi lamulo lake, Ayuda anali ndi chisoni kwambiri ndipo ankasala kudya+ komanso kulira mofuula. Ambiri ankagona paziguduli ndi paphulusa.+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:3 Nsanja ya Olonda,3/15/1986, tsa. 24
3 Ndipo mʼzigawo zonse+ kumene kunafika mawu a mfumu ndi lamulo lake, Ayuda anali ndi chisoni kwambiri ndipo ankasala kudya+ komanso kulira mofuula. Ambiri ankagona paziguduli ndi paphulusa.+