-
Esitere 4:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Atsikana otumikira Mfumukazi Esitere ndiponso amuna ofulidwa amene ankamuyangʼanira atabwera nʼkudzamuuza zimenezi, zinamukhudza kwambiri. Choncho anatumiza zovala kuti Moredikayi akavale mʼmalo mwa zigudulizo, koma Moredikayi anakana.
-