Esitere 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Moredikayi anauza Hataki zonse zimene zinamuchitikira. Anamuuzanso zokhudza ndalama zonse+ zimene Hamani analonjeza kuti apereka mosungiramo chuma cha mfumu, nʼcholinga choti aphe Ayuda.+
7 Moredikayi anauza Hataki zonse zimene zinamuchitikira. Anamuuzanso zokhudza ndalama zonse+ zimene Hamani analonjeza kuti apereka mosungiramo chuma cha mfumu, nʼcholinga choti aphe Ayuda.+