-
Esitere 4:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Anamupatsanso kalata imene munali lamulo lochokera ku Susani*+ loti Ayuda onse aphedwe. Anamupatsa kalatayi kuti akaonetse Esitere ndiponso akamufotokozere mmene zinthu zilili. Moredikayi anauzanso Hataki kuti akauze Esitere+ kuti akaonekere kwa mfumu nʼkupempha kuti imuchitire chifundo ndiponso kuti akachonderere mfumuyo pamasomʼpamaso mʼmalo mwa anthu a mtundu wake.
-