-
Esitere 4:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 “Atumiki onse a mfumu ndi anthu amʼzigawo zonse za mfumu akudziwa kuti, pali lamulo lakuti mwamuna kapena mkazi aliyense wopita mʼbwalo lamkati+ la mfumu asanaitanidwe, ayenera kuphedwa. Munthu saphedwa pokhapokha ngati mfumu yamuloza ndi ndodo yake yagolide.+ Ndiye ine sindinaitanidwe kukaonekera kwa mfumu kwa masiku 30 tsopano.”
-