Esitere 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngati iwe ungakhale chete panopa, thandizo ndi chipulumutso cha Ayuda zichokera kwina.+ Koma iweyo ndi anthu a mʼnyumba ya bambo ako, nonse mudzaphedwa. Ndipo ndani akudziwa? Mwina iwe unakhala mfumukazi kuti uthandize pa nthawi ngati imeneyi.”+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:14 Tsanzirani, tsa. 133 Nsanja ya Olonda,10/1/2011, tsa. 233/15/1986, tsa. 24
14 Ngati iwe ungakhale chete panopa, thandizo ndi chipulumutso cha Ayuda zichokera kwina.+ Koma iweyo ndi anthu a mʼnyumba ya bambo ako, nonse mudzaphedwa. Ndipo ndani akudziwa? Mwina iwe unakhala mfumukazi kuti uthandize pa nthawi ngati imeneyi.”+