Esitere 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa tsiku lachitatu,+ Esitere anavala zovala zachifumu nʼkukaima mʼbwalo lamkati la nyumba ya mfumu kutsogolo kwa nyumba ya mfumuyo. Pa nthawiyi nʼkuti mfumu itakhala pampando wake wachifumu mʼnyumba yakeyo pafupi ndi khomo la nyumbayo. Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Tsanzirani, ptsa. 125, 135 Nsanja ya Olonda,1/1/2012, tsa. 2410/1/2011, tsa. 18
5 Pa tsiku lachitatu,+ Esitere anavala zovala zachifumu nʼkukaima mʼbwalo lamkati la nyumba ya mfumu kutsogolo kwa nyumba ya mfumuyo. Pa nthawiyi nʼkuti mfumu itakhala pampando wake wachifumu mʼnyumba yakeyo pafupi ndi khomo la nyumbayo.