Esitere 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mfumuyo itangoona Mfumukazi Esitere ataima mʼbwalo la nyumba ya mfumu, inasangalala moti inamuloza ndi ndodo yachifumu yagolide+ imene inali mʼmanja mwake. Kenako Esitere anayandikira nʼkugwira kutsogolo kwa ndodoyo. Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:2 Tsanzirani, tsa. 135 Nsanja ya Olonda,1/1/2012, tsa. 24
2 Mfumuyo itangoona Mfumukazi Esitere ataima mʼbwalo la nyumba ya mfumu, inasangalala moti inamuloza ndi ndodo yachifumu yagolide+ imene inali mʼmanja mwake. Kenako Esitere anayandikira nʼkugwira kutsogolo kwa ndodoyo.