Esitere 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa tsikuli Hamani anatuluka ali wosangalala kwambiri. Koma atangoona Moredikayi pageti la mfumu nʼkuonanso kuti sanaimirire ndi kumunjenjemerera, Hamani anamukwiyira kwambiri Moredikayi.+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:9 Tsanzirani, tsa. 139 Nsanja ya Olonda,1/1/2012, ptsa. 25-26
9 Pa tsikuli Hamani anatuluka ali wosangalala kwambiri. Koma atangoona Moredikayi pageti la mfumu nʼkuonanso kuti sanaimirire ndi kumunjenjemerera, Hamani anamukwiyira kwambiri Moredikayi.+