Esitere 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Hamani anaugwira mtima ndipo anapita kunyumba kwake. Kenako anaitanitsa anzake ndi mkazi wake Zeresi.+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:10 Nsanja ya Olonda,8/15/1993, tsa. 20
10 Koma Hamani anaugwira mtima ndipo anapita kunyumba kwake. Kenako anaitanitsa anzake ndi mkazi wake Zeresi.+