Esitere 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Hamani ananenanso kuti: “Kuwonjezera pamenepo, Mfumukazi Esitere sanaitane wina aliyense kuphwando limene anakonza,+ koma anaitana ineyo kuti ndipite ndi mfumu, ndipo mawa wandiitananso pamodzi ndi mfumu.+
12 Hamani ananenanso kuti: “Kuwonjezera pamenepo, Mfumukazi Esitere sanaitane wina aliyense kuphwando limene anakonza,+ koma anaitana ineyo kuti ndipite ndi mfumu, ndipo mawa wandiitananso pamodzi ndi mfumu.+