Esitere 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usiku wa tsiku limenelo mfumu inasowa tulo. Choncho inaitanitsa buku lomwe ankalembamo zochitika za masiku amenewo+ ndipo anayamba kuwerengera mfumu zimene zinalembedwa mʼbukulo. Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:1 Nsanja ya Olonda,3/15/1986, tsa. 28
6 Usiku wa tsiku limenelo mfumu inasowa tulo. Choncho inaitanitsa buku lomwe ankalembamo zochitika za masiku amenewo+ ndipo anayamba kuwerengera mfumu zimene zinalembedwa mʼbukulo.