Esitere 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anapeza kuti mʼbukumo munalembedwa zimene Moredikayi anaulula zokhudza Bigitana ndi Teresi, nduna ziwiri zapanyumba ya mfumu, alonda apakhomo, amene ankafuna kupha Mfumu Ahasiwero.+
2 Anapeza kuti mʼbukumo munalembedwa zimene Moredikayi anaulula zokhudza Bigitana ndi Teresi, nduna ziwiri zapanyumba ya mfumu, alonda apakhomo, amene ankafuna kupha Mfumu Ahasiwero.+