Esitere 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako mfumu inati: “Kodi pabwalopo pali ndani?” Pa nthawiyi nʼkuti Hamani atafika pabwalo lakunja+ la nyumba ya mfumu kudzakambirana ndi mfumuyo zoti Moredikayi apachikidwe pamtengo umene anamukonzera.+
4 Kenako mfumu inati: “Kodi pabwalopo pali ndani?” Pa nthawiyi nʼkuti Hamani atafika pabwalo lakunja+ la nyumba ya mfumu kudzakambirana ndi mfumuyo zoti Moredikayi apachikidwe pamtengo umene anamukonzera.+