Esitere 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Hamani atalowa, mfumu inamufunsa kuti: “Kodi tingamuchitire chiyani munthu amene mfumu ikufuna kumupatsa ulemu?” Hamani atamva zimenezi anaganiza kuti: “Kodi winanso ndani amene mfumu ingafune kumupatsa ulemu kuposa ine?”+
6 Hamani atalowa, mfumu inamufunsa kuti: “Kodi tingamuchitire chiyani munthu amene mfumu ikufuna kumupatsa ulemu?” Hamani atamva zimenezi anaganiza kuti: “Kodi winanso ndani amene mfumu ingafune kumupatsa ulemu kuposa ine?”+