Esitere 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ali mkati mokambirana nkhaniyi, nduna zakunyumba ya mfumu zinafika, ndipo nthawi yomweyo zinatenga Hamani nʼkupita naye kuphwando limene Esitere anakonza.+
14 Ali mkati mokambirana nkhaniyi, nduna zakunyumba ya mfumu zinafika, ndipo nthawi yomweyo zinatenga Hamani nʼkupita naye kuphwando limene Esitere anakonza.+