Esitere 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa tsiku lachiwiri la phwando, pamene ankamwa vinyo, mfumu inafunsanso Esitere kuti: “Ukufuna chiyani Mfumukazi Esitere? Chilichonse chimene ukufuna ndikupatsa. Ukufuna kupempha chiyani? Ngakhale utapempha hafu ya ufumu wangawu, ndikupatsa.”+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:2 Tsanzirani, tsa. 140 Nsanja ya Olonda,1/1/2012, tsa. 26
2 Pa tsiku lachiwiri la phwando, pamene ankamwa vinyo, mfumu inafunsanso Esitere kuti: “Ukufuna chiyani Mfumukazi Esitere? Chilichonse chimene ukufuna ndikupatsa. Ukufuna kupempha chiyani? Ngakhale utapempha hafu ya ufumu wangawu, ndikupatsa.”+