Esitere 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mfumukazi Esitere anayankha kuti: “Ngati mungandikomere mtima mfumu, ndiponso ngati mungandichitire chifundo, ndikupempha kuti mupulumutse moyo wanga komanso muteteze anthu a mtundu wanga.+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:3 Tsanzirani, ptsa. 140-141 Nsanja ya Olonda,1/1/2012, ptsa. 26-27
3 Mfumukazi Esitere anayankha kuti: “Ngati mungandikomere mtima mfumu, ndiponso ngati mungandichitire chifundo, ndikupempha kuti mupulumutse moyo wanga komanso muteteze anthu a mtundu wanga.+