Esitere 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndi anthu a mtundu wanga tagulitsidwa+ kuti tonse tiphedwe.+ Tikanagulitsidwa kuti tikhale akapolo aamuna ndi aakazi, sindikanalankhula kanthu. Koma musalole kuti tsoka limeneli lichitike, chifukwa libweretsanso mavuto kwa inu mfumu.” Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:4 Tsanzirani, tsa. 141 Nsanja ya Olonda,1/1/2012, tsa. 273/1/2006, tsa. 113/15/1986, tsa. 28
4 Ine ndi anthu a mtundu wanga tagulitsidwa+ kuti tonse tiphedwe.+ Tikanagulitsidwa kuti tikhale akapolo aamuna ndi aakazi, sindikanalankhula kanthu. Koma musalole kuti tsoka limeneli lichitike, chifukwa libweretsanso mavuto kwa inu mfumu.”