-
Esitere 7:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndiyeno mfumu inanyamuka paphwandolo itakwiya kwambiri nʼkupita kumunda wamaluwa wapanyumba ya mfumu. Zitatero Hamani ananyamuka kuti achonderere Mfumukazi Esitere kuti ipulumutse moyo wake, chifukwa anadziwa kuti mfumu yatsimikiza kuti imupatse chilango.
-