-
Esitere 7:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kenako mfumu inabwera kuchokera kumunda wamaluwa uja nʼkulowanso mʼnyumba imene munali phwando la vinyo. Ndipo inapeza Hamani atadzigwetsa pampando wokhala ngati bedi pamene panali Esitere. Choncho mfumu inati: “Kodi akufunanso kugwirira mfumukazi mʼnyumba mwanga momwe?” Mfumu itangolankhula zimenezi, anthu anamuphimba nkhope Hamani.
-