11 Mʼmakalatawo mfumu inapereka chilolezo kwa Ayuda mʼmizinda yosiyanasiyana kuti asonkhane nʼcholinga choti adziteteze komanso aphe asilikali a gulu lililonse kapena chigawo chilichonse amene angawaukire, kuphatikizapo akazi ndi ana nʼkutenga zinthu zawo.+