Esitere 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mʼzigawo zonse ndiponso mʼmizinda yonse kumene lamulo la mfumu linafika, Ayuda ankasangalala, kukondwera ndiponso kuchita phwando komanso zikondwerero. Anthu ambiri amʼdzikomo anayamba kunena kuti ndi Ayuda+ chifukwa ankaopa kwambiri Ayudawo. Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:17 Nsanja ya Olonda,3/1/2006, tsa. 113/15/1986, tsa. 28
17 Mʼzigawo zonse ndiponso mʼmizinda yonse kumene lamulo la mfumu linafika, Ayuda ankasangalala, kukondwera ndiponso kuchita phwando komanso zikondwerero. Anthu ambiri amʼdzikomo anayamba kunena kuti ndi Ayuda+ chifukwa ankaopa kwambiri Ayudawo.