Esitere 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zinthu zonse zimene anachita chifukwa cha mphamvu zake, ndiponso mphamvu zonse za Moredikayi+ zimene anapatsidwa ndi mfumu,+ zinalembedwa mʼbuku la mbiri+ ya mafumu a Mediya ndi Perisiya.+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:2 Nsanja ya Olonda,3/15/2009, tsa. 32
2 Zinthu zonse zimene anachita chifukwa cha mphamvu zake, ndiponso mphamvu zonse za Moredikayi+ zimene anapatsidwa ndi mfumu,+ zinalembedwa mʼbuku la mbiri+ ya mafumu a Mediya ndi Perisiya.+