-
Esitere 10:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Moredikayi Myuda anali wachiwiri kwa Mfumu Ahasiwero. Iye anali wamkulu pakati pa Ayuda ndipo abale ake ambiri ankamulemekeza. Moredikayi ankachitira zabwino anthu a mtundu wake ndipo ankaonetsetsa kuti mbadwa zawo zinthu zidzawayendere bwino.
-