Yobu 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwana wake aliyense wamwamuna ankakonza phwando kunyumba kwake pa tsiku limene wasankha.* Iwo ankaitana azichemwali awo atatu kuti adzadye ndi kumwera limodzi. Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:4 Nsanja ya Olonda,3/15/2006, tsa. 13
4 Mwana wake aliyense wamwamuna ankakonza phwando kunyumba kwake pa tsiku limene wasankha.* Iwo ankaitana azichemwali awo atatu kuti adzadye ndi kumwera limodzi.