Yobu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi inuyo simwamuteteza pomuikira mpanda?+ Mwatetezanso nyumba yake ndi zinthu zonse zimene ali nazo. Mwadalitsa ntchito ya manja ake+ ndipo ziweto zake zachuluka kwambiri mʼdzikoli. Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:10 Nsanja ya Olonda,11/15/1994, tsa. 11 Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 107-108
10 Kodi inuyo simwamuteteza pomuikira mpanda?+ Mwatetezanso nyumba yake ndi zinthu zonse zimene ali nazo. Mwadalitsa ntchito ya manja ake+ ndipo ziweto zake zachuluka kwambiri mʼdzikoli.