Yobu 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Yehova anauza Satana kuti: “Chabwino, chilichonse chimene ali nacho chili mʼmanja mwako. Koma dzanja lako lisakhudze munthuyo.” Zitatero Satana anachoka pamaso pa Yehova.+
12 Kenako Yehova anauza Satana kuti: “Chabwino, chilichonse chimene ali nacho chili mʼmanja mwako. Koma dzanja lako lisakhudze munthuyo.” Zitatero Satana anachoka pamaso pa Yehova.+