-
Yobu 1:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kenako Asabeya anabwera nʼkutiukira ndipo analanda ziweto nʼkupha atumiki anu ndi lupanga. Ine ndekha ndi amene ndapulumuka, choncho ndabwera kudzakuuzani uthengawu.”
-