-
Yobu 1:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Asanamalize kulankhula, kunabwera munthu winanso kudzanena kuti: “Ana anu aamuna ndi aakazi amadya komanso kumwa vinyo mʼnyumba ya mchimwene wawo wamkulu.
-