-
Yobu 1:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Mwadzidzidzi kunabwera chimphepo kuchokera mʼchipululu ndipo chinawomba makona 4 a nyumbayo, moti nyumbayo yagwera ana anu nʼkuwapha. Ine ndekha ndi amene ndapulumuka, choncho ndabwera kudzakuuzani uthengawu.”
-