-
Yobu 1:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Yobu atamva zimenezi anaimirira nʼkungʼamba chovala chake ndiponso kumeta tsitsi kumutu kwake. Kenako anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi
-