Yobu 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Satana anachoka pamaso pa Yehova nʼkukachititsa kuti Yobu azunzike ndi zilonda zopweteka,+ kuyambira kuphazi mpaka kumutu. Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:7 Nsanja ya Olonda,11/15/1994, ptsa. 12-13
7 Choncho Satana anachoka pamaso pa Yehova nʼkukachititsa kuti Yobu azunzike ndi zilonda zopweteka,+ kuyambira kuphazi mpaka kumutu.