Yobu 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yobu anamuyankha kuti: “Ukulankhula ngati mmene amalankhulira akazi opusa. Kodi tizingolandira zabwino zokhazokha kuchokera kwa Mulungu woona osalandiranso zoipa?”+ Ngakhale kuti anakumana ndi zonsezi, Yobu sananene chilichonse cholakwika.*+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:10 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 10
10 Koma Yobu anamuyankha kuti: “Ukulankhula ngati mmene amalankhulira akazi opusa. Kodi tizingolandira zabwino zokhazokha kuchokera kwa Mulungu woona osalandiranso zoipa?”+ Ngakhale kuti anakumana ndi zonsezi, Yobu sananene chilichonse cholakwika.*+