Yobu 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atamuona ali chapatali, sanamuzindikire. Kenako anayamba kulira mokweza mawu ndipo anangʼamba zovala zawo nʼkumawaza fumbi mʼmwamba komanso pamutu pawo.+
12 Atamuona ali chapatali, sanamuzindikire. Kenako anayamba kulira mokweza mawu ndipo anangʼamba zovala zawo nʼkumawaza fumbi mʼmwamba komanso pamutu pawo.+