Yobu 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako anakhala pansi limodzi ndi Yobuyo kwa masiku 7 masana ndi usiku. Palibe amene analankhula naye chilichonse chifukwa anaona kuti ululu wake unali waukulu kwambiri.+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:13 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,3/15/2006, tsa. 1411/15/1994, tsa. 13
13 Kenako anakhala pansi limodzi ndi Yobuyo kwa masiku 7 masana ndi usiku. Palibe amene analankhula naye chilichonse chifukwa anaona kuti ululu wake unali waukulu kwambiri.+