-
Yobu 4:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako mzimuwo unaima,
Koma sindinazindikire maonekedwe ake.
Chinthu chinaima pamaso panga.
Kunali bata, kenako ndinamva mawu akuti:
-