-
Yobu 5:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Munthu wanjala amadya zimene munthu wopusa wakolola,
Iye amatenga ngakhale zimene zamera paminga,
Ndipo chuma cha munthu wopusayo ndi ana ake chimalandidwa.
-