Yobu 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa nthawi yanjala adzakupulumutsa* ku imfa,Ndipo adzakupulumutsa ku mphamvu ya lupanga pa nthawi yankhondo.
20 Pa nthawi yanjala adzakupulumutsa* ku imfa,Ndipo adzakupulumutsa ku mphamvu ya lupanga pa nthawi yankhondo.