Yobu 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mulungu adzakuteteza ku lilime lomenya ngati chikwapu,+Ndipo sudzachita mantha tsoka likadzafika.