Yobu 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Miyala yakutchire sidzakuvulaza,*Ndipo nyama zakutchire zidzakhala nawe mwamtendere.