Yobu 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mofanana ndi zimenezi, ndi mmene inu mulili kwa ine.+Mwaona kuopsa kwa mavuto amene ndakumana nawo ndipo mwachita mantha.+
21 Mofanana ndi zimenezi, ndi mmene inu mulili kwa ine.+Mwaona kuopsa kwa mavuto amene ndakumana nawo ndipo mwachita mantha.+