Yobu 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndilangizeni, ndipo ine ndikhala chete.+Ndithandizeni kuti ndimvetse zimene ndalakwitsa.