Yobu 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikagona ndimafunsa kuti, ‘Kodi kucha nthawi yanji?’+ Usikuwo umatalika ndipo ndimangotembenukatembenuka mpaka mʼbandakucha.
4 Ndikagona ndimafunsa kuti, ‘Kodi kucha nthawi yanji?’+ Usikuwo umatalika ndipo ndimangotembenukatembenuka mpaka mʼbandakucha.