Yobu 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho, ine sinditseka pakamwa panga. Ndilankhula chifukwa cha ululu umene ndikumva mumtima mwanga,Ndidandaula mopwetekedwa mtima.+
11 Choncho, ine sinditseka pakamwa panga. Ndilankhula chifukwa cha ululu umene ndikumva mumtima mwanga,Ndidandaula mopwetekedwa mtima.+