Yobu 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngati ndachimwa, kodi zimakukhudzani bwanji, Inu amene mumayangʼanitsitsa anthu?+ Nʼchifukwa chiyani mukulimbana ndi ine? Kodi ndakhala mtolo wolemera kwa inu?
20 Ngati ndachimwa, kodi zimakukhudzani bwanji, Inu amene mumayangʼanitsitsa anthu?+ Nʼchifukwa chiyani mukulimbana ndi ine? Kodi ndakhala mtolo wolemera kwa inu?