Yobu 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi gumbwa* angamere pamalo pamene si padambo? Ndipo kodi bango lingakule popanda madzi?